2 Samueli 19:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo iye anakopa mitima ya anthu onse a Yuda, monga munthu mmodzi, natumiza iwo kwa mfumu, nati, Mubwere inu ndi anyamata anu onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo iye anakopa mitima ya anthu onse a Yuda, monga munthu mmodzi, natumiza iwo kwa mfumu, nati, Mubwere inu ndi anyamata anu onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Choncho Davide adakopa mitima ya Ayuda onse, ndipo adamangana chimodzi. Motero anthuwo adatumiza mau kwa mfumu kuti, “Bwererani inu pamodzi ndi ankhondo anu onse.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Davide anakopa mitima ya anthu onse a Yuda ndipo anthuwo anakhala ngati munthu mmodzi. Iwo anatumiza mawu kwa mfumu, “Bwererani inu ndi anthu anu onse.” Onani mutuwo |