2 Samueli 19:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo anauza Yowabu, Onani mfumu ilikulira misozi, nilira Abisalomu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo anauza Yowabu, Onani mfumu ilikulira misozi, nilira Abisalomu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Anthu ena adauza Yowabu kuti, “Amfumutu akulira maliro a Abisalomu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yowabu anawuzidwa kuti, “Mfumu ikulira maliro a Abisalomu.” Onani mutuwo |