2 Samueli 18:6 - Buku Lopatulika6 Chomwecho anthuwo anatulukira kuthengo kukamenyana ndi Israele; nalimbana ku nkhalango ya ku Efuremu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Chomwecho anthuwo anatulukira kuthengo kukamenyana ndi Israele; nalimbana ku nkhalango ya ku Efuremu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tsono ankhondo adatuluka kunka ku thengo kukamenyana ndi Aisraele. Ndipo nkhondo idachitikira ku nkhalango ya Efuremu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ankhondo anayenda kupita kukachita nkhondo ndi Israeli, ndipo nkhondo inachitika mʼnkhalango ya Efereimu. Onani mutuwo |