2 Samueli 18:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo mfumu inati, Patuka nuime apa. Napatuka, naimapo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo mfumu inati, Patuka nuime apa. Napatuka, naimapo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Pompo mfumu idati, “Patuka, kaime apo.” Iye adapatuka nakaima potero. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Mfumu inati, “Ima apo ndipo udikire.” Kotero iye anapita pa mbali nayima pamenepo. Onani mutuwo |