2 Samueli 18:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo mlondayo anaona munthu wina wothamanga; mlonda naitana wakuchipata nanena, Taona munthu wina wakuthamanga yekha. Ndipo mfumu inati, Iyenso abwera ndi mau. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo mlondayo anaona munthu wina wothamanga; mlonda naitana wakuchipata nanena, Taona munthu wina wakuthamanga yekha. Ndipo mfumu inati, Iyenso abwera ndi mau. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Mlondayo adaona munthu winanso akuthamanga. Ndipo adafuulira munthu wapachipata nati, “Onani, pali munthu winanso akuthamanga yekhayekha.” Apo mfumu idati, “Iyeyonso akubwera ndi nkhani yabwino.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Mlonda uja anaonanso munthu wina akuthamanga, ndipo anayitana woyangʼanira pa chipata, “Taona, munthu winanso akuthamanga ali yekha!” Mfumu inati, “Iye akubweretsanso nkhani yabwino.” Onani mutuwo |