2 Samueli 18:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo anatenga Abisalomu namponya m'chidzenje chachikulu kunkhalangoko; naunjika pamwamba pake mulu waukulu ndithu wamiyala; ndipo Aisraele onse anathawa yense ku hema wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo anatenga Abisalomu namponya m'chidzenje chachikulu kunkhalangoko; naunjika pamwamba pake mulu waukulu ndithu wamiyala; ndipo Aisraele onse anathawa yense ku hema wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Ndipo ankhondowo adatenga mtembo wa Abisalomu, nakautaya m'chidzenje chachikulu m'nkhalango, naunjika mulu wa miyala padzenjepo. Aisraele onse adathaŵa, aliyense kuthaŵira kwao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Iwo anatenga Abisalomu ndi kumuponya mʼdzenje lalikulu mʼchipululumo ndipo anawunjikapo miyala ikuluikulu. Nthawiyi Aisraeli onse anathawa kupita ku nyumba zawo. Onani mutuwo |