2 Samueli 18:18 - Buku Lopatulika18 Koma Abisalomu akali moyo adatenga nadziutsira choimiritsacho chili m'chigwa cha mfumu; pakuti anati, Ndilibe mwana wamwamuna adzakhala chikumbutso cha dzina langa; natcha choimiritsacho ndi dzina la iye yekha; ndipo chitchedwa chikumbutso cha Abisalomu, kufikira lero lomwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Koma Abisalomu akali moyo adatenga nadziutsira choimiritsacho chili m'chigwa cha mfumu; pakuti anati, Ndilibe mwana wamwamuna adzakhala chikumbutso cha dzina langa; natcha choimiritsacho ndi dzina la iye yekha; ndipo chitchedwa chikumbutso cha Abisalomu, kufikira lero lomwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Abisalomu akadali moyo, adaadzimangira chipilala m'chigwa cha mfumu, poti ankati, “Ine ndilibe mwana wamwamuna woti adzakhale chikumbutso cha dzina langa.” Adaatchula chipilalacho dzina lake lomwe, ndipo mpaka pano chikutchulidwa kuti chikumbutso cha Abisalomu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Abisalomu ali ndi moyo anadzimangira chipilala mʼchigwa cha mfumu, pakuti ankaganiza kuti, “Ine ndilibe mwana wamwamuna amene adzakhale chikumbutso changa.” Chipilalacho anachitchula dzina lake lomwe ndipo mpaka lero chimatchedwa chipilala cha Abisalomu. Onani mutuwo |