Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 18:16 - Buku Lopatulika

16 Ndipo Yowabu analiza lipenga, ndipo anthu anabwerera naleka kupirikitsa Aisraele; pakuti Yowabu analetsa anthuwo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Ndipo Yowabu analiza lipenga, ndipo anthu anabwerera naleka kupirikitsa Aisraele; pakuti Yowabu analetsa anthuwo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Pambuyo pake Yowabu adaliza lipenga loletsa nkhondo, ndipo ankhondo ake adabwerako kumene ankalondola Aisraele kuja.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Kenaka Yowabu analiza lipenga ndipo asilikali analeka kuthamangitsa Israeli pakuti Yowabu anawaletsa.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 18:16
6 Mawu Ofanana  

Ndipo anyamata khumi onyamula zida zake za Yowabu anamzungulira Abisalomu namkantha namupha.


Chomwecho Yowabu anaomba lipenga, anthu onse naima, naleka kupirikitsa Aisraele, osaponyana naonso.


Pomwepo mkaziyo anapita kwa anthu onse mwa nzeru yake. Ndipo iwo anadula mutu wa Sheba mwana wa Bikiri, nauponya kunja kwa Yowabu. Ndipo analiza lipenga, nabalalika kuchoka mumzindamo, munthu yense kunka ku hema wake. Ndipo Yowabu anabwerera kunka ku Yerusalemu kwa mfumu.


Pakuti ngati lipenga lipereka mau osazindikirika, adzadzikonzera ndani kunkhondo?


Pamene amuna a Israele anaona kuti adafa Abimeleki anamuka yense kumalo kwake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa