2 Samueli 18:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo anyamata khumi onyamula zida zake za Yowabu anamzungulira Abisalomu namkantha namupha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo anyamata khumi onyamula zida zake za Yowabu anamzungulira Abisalomu namkantha namupha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Pomwepo ankhondo khumi onyamula zida zankhondo za Yowabu, adazinga Abisalomu, namkantha mpaka kumupha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Ndipo anthu khumi onyamula zida za Yowabu anazungulira Abisalomu, kumubaya ndi kumupha. Onani mutuwo |