2 Samueli 18:13 - Buku Lopatulika13 Ndikadachita chonyenga pa moyo wake, palibe mlandu ubisika kwa mfumu; ndipo inu nomwe mukadanditsutsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndikadachita chonyenga pa moyo wake, palibe mlandu ubisika kwa mfumu; ndipo inu nomwe mukadanditsutsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Bwenzi nditanyoza mau a mfumuwo, pomupha mwana wake, ndipo zikadadziŵika, poti palibe kanthu kobisika pamaso pa mfumu, ndipo inu nomwe simukadanditeteza.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ndipo sindikanayika moyo wanga pa chiswe pakuti palibe chimene chimabisika pamaso pa mfumu komanso inu simukanditeteza.” Onani mutuwo |