2 Samueli 17:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo Israele ndi Abisalomu anamanga zithando m'dziko la Giliyadi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo Israele ndi Abisalomu anamanga zithando m'dziko la Giliyadi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Tsono Aisraele pamodzi ndi Abisalomu adamanga zithando zankhondo m'dziko la Giliyadi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Aisraeli ndi Abisalomu anamanga zithando mʼdziko la Giliyadi. Onani mutuwo |