2 Samueli 17:13 - Buku Lopatulika13 Ndiponso ngati walowa kumzinda wina, Aisraele onse adzabwera ndi zingwe kumzindako, ndipo tidzaukokera kumtsinje, kufikira sikapezeka kamwala kakang'ono kumeneko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndiponso ngati walowa kumudzi wina, Aisraele onse adzabwera ndi zingwe kumudziko, ndipo tidzaukokera kumtsinje, kufikira sikapezeka kamwala kakang'ono kumeneko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Akakaloŵa mumzinda mwina, Aisraele onse adzabwera ndi zingwe kumzindako. Mzinda umenewo tidzauguzira ku chigwa, ndipo sipadzapezeka ndi kamwala komwe kumeneko.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Iye akakathawira mu mzinda, Aisraeli onse adzabweretsa zingwe ku mzindawo, ndipo ife tidzawugwetsera ku chigwa mpaka sipadzapezeka ngakhale kachidutswa.” Onani mutuwo |