2 Samueli 17:12 - Buku Lopatulika12 Chomwecho tidzamvumbulukira pamalo akuti adzapezeka, ndipo tidzamgwera monga mame agwa panthaka, ndipo sitidzasiya ndi mmodzi yense wa iye ndi anthu onse ali naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Chomwecho tidamvumbulukira pa malo akuti adzapezeka, ndipo tidzamgwera monga mame agwa panthaka, ndipo sitidzasiya ndi mmodzi yense wa iye ndi anthu onse ali naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Tsono ife tidzampeza Davide kulikonse kumene adzapezeke, ndipo tidzamthira nkhondo monga m'mene mame amagwera ponseponse pa nthaka. Sipadzapulumuka ndi munthu mmodzi yemwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ndipo ife tidzapita kukamuthira nkhondo kulikonse kumene tikamupeze, ndipo ife tikamuthira nkhondo ngati mame pa nthaka. Palibe amene adzakhale wamoyo kaya iye kapena ankhondo ake. Onani mutuwo |