2 Samueli 16:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo Abisalomu, ndi anthu onse aamuna a Israele, anafika ku Yerusalemu, ndi Ahitofele pamodzi naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo Abisalomu, ndi anthu onse amuna a Israele, anafika ku Yerusalemu, ndi Ahitofele pamodzi naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Abisalomu ndi Aisraele onse amene anali naye, kudzanso Ahitofele, adaaloŵa mu Yerusalemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Pa nthawi imeneyi Abisalomu ndi Aisraeli ena onse anabwera ku Yerusalemu, Ahitofele anali naye. Onani mutuwo |