2 Samueli 16:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo mfumu ndi anthu onse amene anali naye anafika olema; ndipo iye anadzitsitsimutsa kumeneko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo mfumu ndi anthu onse amene anali naye anafika olema; ndipo iye anadzitsitsimutsa kumeneko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Tsono mfumu ndi anthu onse amene anali naye, adafika ku Yordani ali otopa kwambiri, napumula kumeneko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Mfumu ndi anthu ake onse anafika kumene amapita atatopa kwambiri. Ndipo kumeneko anapumula. Onani mutuwo |