2 Samueli 16:13 - Buku Lopatulika13 Chomwecho Davide ndi anthu ake anapita m'njira, ndipo Simei analambalala paphiri popenyana naye, namuka natukwana, namponya miyala, nawaza fumbi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Chomwecho Davide ndi anthu ake anapita m'njira, ndipo Simei analambalala paphiri popenyana naye, namuka natukwana, namponya miyala, nawaza fumbi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Motero Davide ndi anthu ake ankayenda mu mseu pamene Simei ankapita mbali inai m'mphepete mwa phiri, kutukwana kuli m'kati. Ndipo ankaponya miyala Davide ndi kumamuwazanso dothi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Kotero Davide ndi anthu ake anapitirira kuyenda mu msewu pamene Simei amayenda mʼmbali mwa phiri moyangʼanana naye akutukwana ndi kuponya miyala pamene amayenda nʼkumamutsiranso dothi. Onani mutuwo |