2 Samueli 16:12 - Buku Lopatulika12 Kapena Yehova adzayang'anira chosayenerachi alikundichitira ine, ndipo Yehova adzandibwezera chabwino m'malo mwa kunditukwana kwa lero. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Kapena Yehova adzayang'anira chosayenerachi alikundichitira ine, ndipo Yehova adzandibwezera chabwino m'malo mwa kunditukwana kwa lero. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Mwina mwake Chauta adzaona mavuto anga, nadzandibwezera zabwino chifukwa cha kunditukwanaku.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Mwina Yehova adzaona mazunzo anga ndipo adzandibwezera zabwino chifukwa cha kutukwanidwa kumene ndikulandira lero.” Onani mutuwo |