Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 15:9 - Buku Lopatulika

9 Ndipo mfumu inanena naye, Muka ndi mtendere. Chomwecho ananyamuka, nanka ku Hebroni.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo mfumu inanena naye, Muka ndi mtendere. Chomwecho ananyamuka, nanka ku Hebroni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Apo mfumu idamuuza kuti, “Upite ndi mtendere.” Choncho Abisalomu adanyamuka napita ku Hebroni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Mfumu inati kwa iye, “Pita mu mtendere” Kotero iye anapita ku Hebroni.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 15:9
5 Mawu Ofanana  

Koma Abisalomu anatumiza ozonda ku mafuko onse a Israele, kuti, Pakumva kulira kwa lipenga, pomwepo muzinena, Abisalomu ali mfumu ku Hebroni.


Pakuti mnyamata wanu ndinawinda pakukhala ine ku Gesuri mu Aramu, ndi kuti, Yehova akadzandibwezeranso ndithu ku Yerusalemu, ine ndidzatumikira Yehova.


Ndipo Yoswa ndi Aisraele onse naye anakwera kuchokera ku Egiloni mpaka ku Hebroni, nauthira nkhondo;


Pamenepo Eli anayankha nati, Pita ndi mtendere; ndipo Mulungu wa Israele akupatse chopempha chako unachipempha kwa Iye.


Chomwecho Davide analandira m'dzanja lake zimene iye anamtengera; nanena naye, Ukwere kwanu mumtendere; ona, ndamvera mau ako, ndavomereza nkhope yako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa