Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 15:9 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Mfumu inati kwa iye, “Pita mu mtendere” Kotero iye anapita ku Hebroni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

9 Ndipo mfumu inanena naye, Muka ndi mtendere. Chomwecho ananyamuka, nanka ku Hebroni.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo mfumu inanena naye, Muka ndi mtendere. Chomwecho ananyamuka, nanka ku Hebroni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Apo mfumu idamuuza kuti, “Upite ndi mtendere.” Choncho Abisalomu adanyamuka napita ku Hebroni.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 15:9
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Abisalomu anatuma amithenga ake mwamseri kwa mafuko onse a Israeli kukanena kuti, “Mukangomva kulira kwa malipenga pamenepo munene kuti, ‘Abisalomu ndiye mfumu mu Hebroni.’ ”


Pamene mtumiki wanu amakhala ku Gesuri ku Aramu, anachita lonjezo ili: ‘Ngati Yehova adzandibweretsadi ku Yerusalemu, ndidzapembedza Yehovayo mu Hebroni.’ ”


Kenaka Yoswa ndi Aisraeli onse anachoka ku Egiloni nakafika ku Hebroni ndi kukawuthira nkhondo.


Eli anayankha, “Pitani mu mtendere, ndipo Mulungu wa Israeli akupatseni zimene mwamupemphazo.”


Ndipo Davide analandira kwa mayiyo zimene anamutengera ndipo anati, “Pitani kwanu mu mtendere. Ine ndamva mawu anu ndipo ndavomera zimene mwapempha.”


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa