Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 15:37 - Buku Lopatulika

37 Chomwecho Husai bwenzi la Davide anadza m'mzindamo; ndipo Abisalomu anafika ku Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

37 Chomwecho Husai bwenzi la Davide anadza m'mudzimo; ndipo Abisalomu anafika ku Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

37 Choncho Husai, bwenzi la Davide, adaloŵa mu mzinda, nthaŵi yomwe Abisalomu ankaloŵa mu Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

37 Ndipo Husai bwenzi la Davide anafika ku Yerusalemu pamene Abisalomu amalowa mu mzinda.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 15:37
5 Mawu Ofanana  

Pomwepo Abisalomu anati, Kaitane tsopano Husai Mwariki yemwe, timvenso chimene anene iye.


ndi Azariya mwana wa Natani anayang'anira akapitao, ndipo Zabudi mwana wa Natani anali wansembe ndi nduna yopangira mfumu,


ndi Ahitofele anali phungu wa mfumu, ndi Husai Mwariki anali bwenzi la mfumu;


natuluka ku Betele kunka ku Luzi, napitirira kunka ku malire a Aariki, ku Ataroti;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa