2 Samueli 15:35 - Buku Lopatulika35 Ndipo suli nao kumeneko Zadoki ndi Abiyatara ansembewo kodi? Motero chilichonse udzachimva cha m'nyumba ya mfumu uziuza Zadoki ndi Abiyatara ansembewo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Ndipo suli nao kumeneko Zadoki ndi Abiyatara ansembewo kodi? Motero chilichonse udzachimva cha m'nyumba ya mfumu uziuza Zadoki ndi Abiyatara ansembewo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Kodi Zadoki ndi Abiyatara si ansembe amene ali nawe kumeneko? Tsono chilichonse chimene ungachimve kunyumba kwa mfumu, ukaŵauze ansembe amenewo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Kodi ansembe, Zadoki ndi Abiatara, sakukhala nawe kumeneko? Ukawawuze zonse zimene umamva mʼnyumba yaufumu. Onani mutuwo |