2 Samueli 15:3 - Buku Lopatulika3 Abisalomu nanena naye, Ona zokamba zako ndizo zabwino ndi zolungama; koma mfumu sinauze wina kuti adzamve za iwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Abisalomu nanena naye, Ona zokamba zako ndizo zabwino ndi zolungama; koma mfumu sinauze wina kuti adzamve za iwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Abisalomu ankamuuza kuti, “Taona, zimene ukunenazi nzabwino ndi zolungama. Koma mfumu sidaike munthu woti azimva madandaulo anu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Kenaka Abisalomu amanena kwa iye kuti, “Taona, madandawulo ako ndi abwino ndi oyenera, koma palibe woyimira mfumu woti akumvere.” Onani mutuwo |