2 Samueli 15:28 - Buku Lopatulika28 Ona ndidzaima pa madooko a m'chipululu kufikira afika mau ako akunditsimikizira ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ona ndidzaima pa madooko a m'chipululu kufikira afika mau ako akunditsimikizira ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Tsono ine ndidzadikira ku madooko a Yordani ku chipululu mpaka nditalandira mau ochokera kwa inu ondiwuza m'mene ziliri zinthu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Ine ndidzadikira powolokera Yorodani ku chipululu mpaka nditalandira mawu ochokera kwa iwe ondiwuza mmene zilili zinthu.” Onani mutuwo |