2 Samueli 15:29 - Buku Lopatulika29 Chifukwa chake Zadoki ndi Abiyatara ananyamulanso likasa la Mulungu nafika nalo ku Yerusalemu. Ndipo iwo anakhala kumeneko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Chifukwa chake Zadoki ndi Abiyatara ananyamulanso likasa la Mulungu nafika nalo ku Yerusalemu. Ndipo iwo anakhala kumeneko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Pamenepo Zadoki ndi Abiyatara adanyamula Bokosi lija nabwerera nalo ku Yerusalemu, ndipo adakakhala kumeneko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Kotero Zadoki ndi Abiatara ananyamula Bokosi la Mulungu lija nabwerera nalo ku Yerusalemu, ndipo anakakhala kumeneko. Onani mutuwo |