2 Samueli 15:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo Davide ananena ndi Itai, Tiye nuoloke. Ndipo Itai Mgiti anaoloka, ndi anthu ake onse, ndi ana aang'ono onse amene anali naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo Davide ananena ndi Itai, Tiye nuoloke. Ndipo Itai Mgiti anaoloka, ndi anthu ake onse, ndi ana ang'ono onse amene anali naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Choncho Davide adauza Itai kuti, “Chabwino, tiye.” Motero Itai Mgiti uja adaoloka mtsinje wa Kidroni, pamodzi ndi anthu ake, akuluakulu ndi ang'onoang'ono omwe amene anali naye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Davide anati kwa Itai, “Tiye pita nafe” Kotero Itai Mgiti anayenda pamodzi ndi anthu ake ndi mabanja amene anali naye. Onani mutuwo |