2 Samueli 14:20 - Buku Lopatulika20 Mnyamata wanu Yowabu anachita chinthu ichi kuti asandulize mamvekedwe a mlanduwo. Ndipo mbuye wanga ali wanzeru, monga ndi nzeru ya mthenga wa Mulungu, kudziwa zonse zili m'dziko lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Mnyamata wanu Yowabu anachita chinthu ichi kuti asandulize mamvekedwe a mlanduwo. Ndipo mbuye wanga ali wanzeru, monga ndi nzeru ya mthenga wa Mulungu, kudziwa zonse zili m'dziko lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Mtumiki wanu Yowabu adachita zimenezi kuti asinthe mayendedwe ake a zinthu. Koma inu mbuyanga muli ndi nzeru zonga za mngelo wa Mulungu, mutha kudziŵa zinthu zonse za pa dziko lapansi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Mtumiki wanu Yowabu anachita zimenezi kuti asinthe mmene zinthu zilili lero. Mbuye wanga muli ndi nzeru ngati za mngelo wa Mulungu. Mumadziwa zonse zimene zikuchitika mʼdziko.” Onani mutuwo |