2 Samueli 14:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo mfumuyo inanena ndi Yowabu, Taonanitu, ndachita chinthu ichi; chifukwa chake, pita nubwere nayenso mnyamatayo Abisalomu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo mfumuyo inanena ndi Yowabu, Taonanitu, ndachita chinthu ichi; chifukwa chake, pita nubwere nayenso mnyamatayo Abisalomu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Pambuyo pake mfumu idauza Yowabu kuti, “Chabwino tsono, ndavomera kuti zimenezi zichitike. Pita, kamtenge mnyamata uja Abisalomu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Mfumu inati kwa Yowabu, “Chabwino, ine ndichita zimenezi. Pita kamutenge Abisalomuyo.” Onani mutuwo |