2 Samueli 14:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Yowabu mwana wa Zeruya anazindikira kuti mtima wa mfumu unalunjika kwa Abisalomu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Yowabu mwana wa Zeruya anazindikira kuti mtima wa mfumu unalunjika kwa Abisalomu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Yowabu, mwana wa Zeruya, adaadziŵa kuti mtima wa mfumu uli pa Abisalomu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yowabu mwana wa Zeruya anadziwa kuti maganizo a mfumu ali pa Abisalomu. Onani mutuwo |