2 Samueli 13:39 - Buku Lopatulika39 Ndipo mfumu Davide analira kunka kwa Abisalomu, chifukwa anasangalatsidwa pa imfa ya Aminoni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Ndipo mfumu Davide analira kunka kwa Abisalomu, chifukwa anasangalatsidwa pa imfa ya Aminoni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Tsono mfumu Davide adagwidwa ndi chifundo chofuna kumlondola Abisalomuyo. Pamenepo nkuti Davideyo atatonthozedwa pa imfa ya Aminoni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Ndipo Davide anagwidwa ndi chifundo chofuna kumulondola Abisalomu pakuti anali atatonthozedwa pa imfa ya Amnoni. Onani mutuwo |