Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 13:27 - Buku Lopatulika

27 Koma Abisalomu anaiumirira iyo, nilola kuti Aminoni ndi ana aamuna onse a mfumu apite naye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

27 Koma Abisalomu anaiumirira iyo, nilola kuti Aminoni ndi ana amuna onse a mfumu apite naye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

27 Koma Abisalomu adamkakamiza ndithu mpaka Davide adalola kuti Aminoni pamodzi ndi ana onse aamuna a mfumu apite nao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

27 Koma Abisalomu anamuwumiriza, kotero analola kuti Amnoni pamodzi ndi ana onse a mfumu apite naye.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 13:27
3 Mawu Ofanana  

Pomwepo Abisalomu anati, Ngati nkutero, mulole mbale wanga Aminoni apite nafe. Ndipo mfumu inanena naye, Iye apitirenji nawe?


Ndipo Abisalomu analamulira anyamata ake, nati, Inu mukhale maso, mtima wa Aminoni ukasekera ndi vinyo, ndipo ine ndikati kwa inu, Kanthani Aminoni; pamenepo mumuphe, musaope; sindine ndakulamulirani inu mulimbike, chitani chamuna.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa