2 Samueli 13:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo mfumu inati kwa Abisalomu, Iai mwana wanga, tisapite tonse, kuti tingakuchulukire. Ndipo iye anaiumirira koma inakana kupita; koma inamdalitsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo mfumu inati kwa Abisalomu, Iai mwana wanga, tisapite tonse, kuti tingakuchulukire. Ndipo iye anaiumirira koma inakana kupita; koma inamdalitsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Koma mfumu idauza Abisalomu kuti, “Iyai, mwana wanga, tisachite kupita tonse, tingakakuvutitse.” Adayesera muno ndi muno kumuumiriza, komabe Davide sadapite nao, m'malo mwake adangomdalitsa Abisalomuyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Mfumu inayankha kuti, “Ayi mwana wanga, tisapite tonsefe. Tidzakhala cholemetsa kwa iwe.” Ngakhale Abisalomu anayesetsa kuwumiriza mfumuyo, inakana kupita. Mʼmalo mwake inangomudalitsa Abisalomuyo. Onani mutuwo |