2 Samueli 13:17 - Buku Lopatulika17 Pomwepo anaitana mnyamata wake amene anamtumikira, nati, Tulutsa mkazi uyu kwa ine, nupiringidze chitseko atapita iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Pomwepo anaitana mnyamata wake amene anamtumikira, nati, Tulutsa mkazi uyu kwa ine, nupiringidze chitseko atapita iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Pomwepo Aminoniyo adaitana mnyamata amene ankamtumikira, namuuza kuti, “Mtulutse mkaziyu, achoke pano, ndisamuwonenso, ndipo upiringidze chitseko iyeyo akatuluka.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Amnoni anayitana wantchito wake ndipo anati, “Mutulutse mkazi uyu muno ndipo utseke chitseko akatuluka.” Onani mutuwo |