Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 13:11 - Buku Lopatulika

11 Ndipo pamene anabwera nato pafupi kuti adye, iye anamgwira, nanena naye, Idza nugone nane, mlongo wanga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo pamene anabwera nato pafupi kuti adye, iye anamgwira, nanena naye, Idza nugone nane, mlongo wanga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Koma atafika nacho chakudyacho pafupi ndi Aminoni kuti adye, Aminoni adamgwira Tamara, namuuza kuti, “Bwera ugone nane, iwe Tamara.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Koma atabweretsa kwa iye kuti adye, anamugwira ndipo anati, “Bwera ugone nane, iwe mlongo wanga.”

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 13:11
4 Mawu Ofanana  

Ndipo panali zitapita izi, kuti mkazi wa mbuyake anamyang'anira maso Yosefe: ndipo mkaziyo anati, Gona ndi ine.


Ndipo Aminoni anati kwa Tamara, Bwera nacho chakudya kuchipinda kuti ndikadye cha m'manja mwako. Ndipo Tamara anatenga timitanda anatipangato, nabwera nato kuchipinda kwa Aminoni mlongo wake.


Ndipo wina anachita chonyansa ndi mkazi wa mnansi wake, winanso wadetsa mpongozi wake mwamanyazi, ndi wina mwa iwe anaipitsa mlongo wake mwana wamkazi wa atate wake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa