2 Samueli 12:28 - Buku Lopatulika28 Chifukwa chake tsono musonkhanitse anthu otsalawo, nimumangire mzindawo zithando, muulande; kuti ine ndingalande mzindawo, ndipo ungatchedwe ndi dzina langa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Chifukwa chake tsono musonkhanitse anthu otsalawo, nimumangire mudziwo zithando, muulande; kuti ine ndingalande mudziwo, ndipo ungatchedwe ndi dzina langa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Tsono inu musonkhanitse ankhondo onse otsala, ndipo bwerani mudzauzinge ndi zithando mzindawo ndi kuulanda, kuwopa kuti ine ndikalanda mzindawo, ungamatchedwe dzina langa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Ndipo tsopano sonkhanitsani asilikali onse ndipo muzungulire mzindawo ndi kuwulanda.” Onani mutuwo |