2 Samueli 12:29 - Buku Lopatulika29 Ndipo Davide anasonkhanitsa anthu onse, napita ku Raba, naponyana nao, naulanda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Ndipo Davide anasonkhanitsa anthu onse, napita ku Raba, naponyana nao, naulanda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Choncho Davide adasonkhanitsa ankhondo ake onse, ndipo adapita ku Raba, nakauthira nkhondo mzindawo, nkuulanda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Kotero Davide anasonkhanitsa ankhondo onse ndipo anapita ku Raba kukawuthira nkhondo ndi kuwulanda. Onani mutuwo |