2 Samueli 12:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo Yowabu anathira nkhondo pa Raba wa ana a Amoni, nalanda mzinda wachifumu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo Yowabu anathira nkhondo pa Raba wa ana a Amoni, nalanda mudzi wachifumu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Nthaŵi imeneyo Yowabu ndi ankhondo a Aisraele ankathira nkhondo Raba, likulu la Aamoni, ndipo anali pafupi kuulanda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Pa nthawi imeneyi Yowabu anamenyana ndi Raba ku Amoni ndipo analanda nsanja yaufumu. Onani mutuwo |