2 Samueli 12:25 - Buku Lopatulika25 natumiza ndi dzanja la Natani mneneriyo, namutcha dzina lake Wokondedwa ndi Yehova, chifukwa cha Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 natumiza ndi dzanja la Natani mneneriyo, namutcha dzina lake Wokondedwa ndi Yehova, chifukwa cha Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 ndipo adatumiza mau kudzera mwa mneneri Natani kuti mwanayo dzina lake likhale Yedidiya, chifukwa Chauta adaamkonda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Ndipo chifukwa chakuti Yehova ankamukonda iyeyo, Yehovayo anatumiza mawu kwa mneneri Natani kuti akamutchule Yedidiya. Onani mutuwo |