2 Samueli 12:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo Davide anasangalatsa Bateseba mkazi wake, nalowa kwa iye, nagona naye; ndipo anabala mwana wamwamuna, namutcha dzina lake Solomoni. Ndipo Yehova anamkonda iye, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo Davide anasangalatsa Bateseba mkazi wake, nalowa kwa iye, nagona naye; ndipo anabala mwana wamwamuna, namutcha dzina lake Solomoni. Ndipo Yehova anamkonda iye, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Tsono Davide adatonthoza mtima wa mkazi wake Bateseba, nakaloŵa kwa mkaziyo. Pambuyo pake mkazi uja adabala mwana wamwamuna, ndipo Davide adamutcha dzina lake Solomoni. Chauta adamkonda mwanayo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Ndipo Davide anatonthoza mkazi wake Batiseba, napita kwa iye ndi kugona naye. Iye anabereka mwana wamwamuna, ndipo anamutcha dzina lake Solomoni. Yehova ankamukonda iye. Onani mutuwo |