Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 12:23 - Buku Lopatulika

23 Koma tsopano wafa, ndidzasaliranjinso kudya? Kodi ndikhoza kumbweza? Ine ndidzamuka kuli iye, koma iye sadzabweranso kwa ine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Koma tsopano wafa, ndidzasaliranjinso kudya? Kodi ndikhoza kumbweza? Ine ndidzamuka kuli iye, koma iye sadzabweranso kwa ine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Koma tsopano mwanayo wafa. Nanga ndizikaniranjinso zakudya? Kodi ndingathe kumbwezanso? Ine ndidzapitadi kumene kuli iyeko, koma iyeyo sadzabwereranso kwa ine.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Koma tsopano wamwalira ndisaliranji chakudya? Kodi ndingathe kumubwezanso? Ine ndidzapita kumene kuli iyeko, koma iye sadzabwerera kwa ine.”

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 12:23
6 Mawu Ofanana  

Ndipo ana aamuna ake onse ndi ana aakazi onse anauka kuti amtonthoze: koma anakana kutonthozedwa; ndipo anati, Pakuti ndidzatsikira kumanda kwa mwana wanga, ndilinkulirabe. Atate wake ndipo anamlirira.


Ndimuka ine njira ya dziko lonse: limba mtima tsono, nudzionetse umunthu;


ndisanachoke kunka kumene sindikabweranso, ku dziko la mdima ndi la mthunzi wa imfa.


Pakuti ndidziwa kuti mudzandifikitsa kuimfa, ndi kunyumba yokomanamo amoyo onse.


Ndipo Iye ananena naye, Indetu, ndinena ndi iwe, Lero lino udzakhala ndine mu Paradaiso.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa