2 Samueli 12:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo akulu a m'nyumba yake ananyamuka, naima pa iye, kuti akamuutse pansi; koma anakana, osafuna kudya nao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo akulu a m'nyumba yake ananyamuka, naima pa iye, kuti akamuutse pansi; koma anakana, osafuna kudya nao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Akuluakulu a ku nyumba ya mfumu adadzaima pambali pake kuti amuutse. Koma iye adakana kuuka, ndipo sadadye nawo chakudya anthuwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Akuluakulu a banja lake anayima pambali pake kuti amudzutse, koma iye anakana, ndipo sanadye chakudya chilichonse pamodzi ndi iwo. Onani mutuwo |