2 Samueli 12:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo Natani anamuka kwao. Ndipo Yehova anadwaza mwana amene mkazi wa Uriya anambalira Davide, nadwala kwambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo Natani anamuka kwao. Ndipo Yehova anadwaza mwana amene mkazi wa Uriya anambalira Davide, nadwala kwambiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Pompo Natani adabwerera kunyumba kwake. Motero Chauta adalanga mwana amene mkazi wa Uriya adabalira Davide, ndipo adadwala kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Natani atapita kwawo, Yehova anakantha mwana amene mkazi wa Uriya anabereka ndipo anayamba kudwala. Onani mutuwo |