2 Samueli 11:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo pamene mkazi wa Uriya anamva kuti Uriya mwamuna wake adamwalira, iye analira maliro a mwamuna wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo pamene mkazi wa Uriya anamva kuti Uriya mwamuna wake adamwalira, iye analira maliro a mwamuna wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Pamene mkazi wa Uriya adamva kuti mwamuna wake Uriya adaphedwa, adalira, kulira mwamuna wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Mkazi wa Uriya atamva kuti mwamuna wake wafa, analira maliro. Onani mutuwo |