2 Samueli 11:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo akumzindawo anatuluka, namenyana ndi Yowabu; ndipo adagwapo anthu ena, ndiwo a anyamata a Davide; ndi Uriya Muhiti anafanso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo akumudziwo anatuluka, namenyana ndi Yowabu; ndipo adagwapo anthu ena, ndiwo a anyamata a Davide; ndi Uriya Muhiti anafanso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Tsono ankhondo amumzindamo adatuluka nadzamenyana ndi Yowabu. Ndipo ena mwa ankhondo a Davide adaphedwa. Uriya, Muhiti uja, nayenso adaphedwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Ankhondo a mu mzindawo atabwera kudzamenyana ndi Yowabu, anthu ena a gulu la ankhondo la Davide anaphedwa ndipo Uriya Mhiti uja anaphedwanso. Onani mutuwo |