2 Samueli 11:18 - Buku Lopatulika18 Pamenepo Yowabu anatumiza munthu nauza Davide zonse za nkhondoyi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Pamenepo Yowabu anatumiza munthu nauza Davide zonse za nkhondoyi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Zitatero, Yowabu adatuma wamthenga kwa Davide kukamuuza zonse zimene zidachitika kunkhondoko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Yowabu anatumiza wamthenga kwa Davide kukafotokoza mwatsatanetsatane za nkhondoyo. Onani mutuwo |