2 Samueli 10:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo pamene Aaramu anaona kuti Aisraele anawathyola, anasonkhana pamodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo pamene Aaramu anaona kuti Aisraele anawathyola, anasonkhana pamodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Koma Asiriya ataona kuti agonjetsedwa ndi Aisraele, adasonkanitsa ankhondo ao onse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Aaramu ataona kuti agonjetsedwa ndi Aisraeli, anasonkhananso. Onani mutuwo |