Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 10:13 - Buku Lopatulika

13 Chomwecho Yowabu ndi anthu amene anali naye anayandikira kuponyana nkhondo ndi Aaramu. Ndipo iwowa anathawa pamaso pake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Chomwecho Yowabu ndi anthu amene anali naye anayandikira kuponyana nkhondo ndi Aaramu. Ndipo iwowa anathawa pamaso pake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Choncho Yowabu ndi anthu ake adasendera pafupi ndi Asiriya aja kuti amenyane nawo nkhondo, koma Asiriyawo adathaŵa iye akufika.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Choncho Yowabu ndi ankhondo amene anali naye anapita kukamenyana ndi Aaramu, ndipo iwo anathawa pamaso pake.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 10:13
6 Mawu Ofanana  

Ndipo pakufika Aaramu a ku Damasiko kudzathandiza Hadadezere mfumu ya ku Zoba, Davide anakanthako Aaramu zikwi makumi awiri mphambu ziwiri.


Muwachotse monga utsi uchotseka; monga phula lisungunuka pamoto, aonongeke oipa pamaso pa Mulungu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa