Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 10:11 - Buku Lopatulika

11 Ndipo iye anati, Aaramu akandipambana ine, udzandithandiza ndiwe, koma ana a Amoni akapambana iwe, tsono ndidzabwera ine kukuthandiza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo iye anati, Aaramu akandipambana ine, udzandithandiza ndiwe, koma ana a Amoni akapambana iwe, tsono ndidzabwera ine kukuthandiza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Tsono Yowabu adauza Abisai kuti, “Ngati Asiriya andipose mphamvu, iweyo udzandithandize. Koma ngati Aamoni akupose mphamvu, ndiye kuti ineyo ndidzabwera kudzakuthandiza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Yowabu anati, “Ngati Aaramu andipose mphamvu, iwe ubwere udzandipulumutse. Koma ngati Aamoni akupose mphamvu, ine ndidzabwera kudzakupulumutsa.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 10:11
8 Mawu Ofanana  

Koma anthu otsalawo anawapereka kwa Abisai mbale wake, amene anawandandalitsa cha kwa Amoni.


Ulimbike mtima, ndipo tichite chamuna lero chifukwa cha anthu athu ndi mizinda ya Mulungu wathu; Yehova nachite chomkomera.


paliponse mukumva mau a lipenga, musonkhanire komweko kwa ife; Mulungu wathu adzatigwirira nkhondo.


koma ndinakupempherera kuti chikhulupiriro chako chingazime; ndipo iwe, pamene watembenuka ukhazikitse abale ako.


Ndipo ife amene tili olimba tiyenera kunyamula zofooka za opanda mphamvu, ndi kusadzikondweretsa tokha.


Nyamuliranani zothodwetsa, ndipo kotero mufitse chilamulo cha Khristu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa