2 Samueli 1:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo anati kwa ine, Uime pa ine nundiphe, chifukwa kuwawa mtima kwandigwera ine, popeza ndikali moyobe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo anati kwa ine, Uime pa ine nundiphe, chifukwa kuwawa mtima kwandigwera ine, popeza ndikali moyobe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Apo adandiwuza kuti, ‘Bwera pafupi, undiphe, chifukwa ndikumva ululu woopsa, komabe ndikali moyo.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “Kenaka iye anati kwa ine, ‘Bwera pafupi ndipo undiphe! Ndikumva ululu kwambiri, koma ndikanali ndi moyo!’ Onani mutuwo |