Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 1:5 - Buku Lopatulika

5 Ndipo Davide ananena ndi mnyamata wakumuuza, Udziwa bwanji kuti Saulo ndi Yonatani mwana wake anafa?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo Davide ananena ndi mnyamata wakumuuza, Udziwa bwanji kuti Saulo ndi Yonatani mwana wake anafa?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Apo Davide adamufunsa mnyamatayo kuti, “Iwe wadziŵa bwanji kuti Saulo ndi Yonatani nawonso adafa?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Ndipo Davide anati kwa mnyamata amene anabweretsa nkhaniyi, “Ukudziwa bwanji kuti Sauli ndi mwana wake Yonatani afa?”

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 1:5
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Davide ananena naye, Kunaonekanji? Undiuze. Nayankha iye, Anthu anathawa kunkhondo, ndipo ambiri anagwa nafa; ndipo Saulo ndi Yonatani mwana wake anafanso.


Mnyamata wakumuuzayo nati, Pamene ndinangoyenda paphiri la Gilibowa, ndinaona, Saulo alikuyedzamira nthungo yake, ndi magaleta ndi apakavalo anamyandikiza.


Wachibwana akhulupirira mau onse; koma wochenjera asamalira mayendedwe ake.


Kubisa kanthu ndi ulemerero wa Mulungu; koma ulemerero wa mafumu ndi kusanthula kanthu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa