2 Samueli 1:22 - Buku Lopatulika22 Uta wa Yonatani sunabwerere, ndipo lupanga la Saulo silinabwerere chabe, pa mwazi wa ophedwa, pa mafuta a amphamvuwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Uta wa Yonatani sunabwerera, ndipo lupanga la Saulo silinabwerera chabe, pa mwazi wa ophedwa, pa mafuta a amphamvuwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 “Uta wa Yonatani sudabwereko chabe osakhetsa magazi a anthu osabayako ankhondo amphamvu. Ndipo lupanga la Saulo silidabwereko chabe osapha anthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 “Pa magazi a ophedwa, pa mnofu wa amphamvu, uta wa Yonatani sunabwerere, lupanga la Sauli silinabwere chabe. Onani mutuwo |